Genesis 29:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo panali pamene Yakobo anaona Rakele, mwana wamkazi wa Labani, mlongo wake wa amake, ndi nkhosa za Labani mlongo wake wa amake, Yakobo anayandikira nagubuduza kuuchotsa mwala pachitsime, nazimwetsa zoweta za Labani, mlongo wake wa amake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo panali pamene Yakobo anaona Rakele, mwana wamkazi wa Labani, mlongo wake wa amake, ndi nkhosa za Labani mlongo wake wa amake, Yakobo anayandikira nagubuduza kuuchotsa mwala pachitsime, nazimwetsa zoweta za Labani, mlongo wake wa amake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Yakobe ataona Rakele ali ndi nkhosa za bambo wake Labani, adapita kuchitsimeko, nakunkhuniza mwalawo, nkuzimwetsa madzi nkhosa za Labanizo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Yakobo ataona Rakele mwana wa Labani, mlongo wa amayi ake, ali ndi nkhosa za Labani, anapita nawugudubuza mwala uja nazimwetsa madzi nkhosa za amalume akezo. Onani mutuwo |