Genesis 29:9 - Buku Lopatulika9 Ali chilankhulire nao, anafika Rakele ndi nkhosa za atate wake, chifukwa anaziweta. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ali chilankhulire nao, anafika Rakele ndi nkhosa za atate wake, chifukwa anaziweta. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Yakobe akulankhulabe ndi iwowo, Rakele adafika ndi nkhosa za atate ake. Iyeyo ndiye ankaŵeta nkhosazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ali chiyankhulire nawo, Rakele anafika ndi nkhosa za abambo ake popeza ndiye amene ankaweta nkhosazo. Onani mutuwo |