Genesis 28:4 - Buku Lopatulika4 akupatse iwe mdalitso wa Abrahamu, iwe ndi mbeu zako pamodzi nawe: kuti ulowe m'dziko limene ukhalamo mlendo, limene Mulungu anampatsa Abrahamu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 akupatse iwe mdalitso wa Abrahamu, iwe ndi mbeu zako pamodzi nawe: kuti ulowe m'dziko limene ukhalamo mlendo, limene Mulungu anampatsa Abrahamu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Akudalitse iwe pamodzi ndi zidzukulu zako monga momwe adadalitsira Abrahamu, kuti lidzakhale lakodi dziko limene ukakhalemolo, dziko limene adapatsa Abrahamu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Mulunguyo akudalitse iwe monga mmene anamudalitsira Abrahamu kuti zidzukulu zako zidzalandira dziko limene ukukhalamo ngati mlendo kuti lidzakhale lawo. Ili ndi dziko limene Mulungu anapereka kwa Abrahamu.” Onani mutuwo |