Genesis 28:3 - Buku Lopatulika3 Mulungu Wamphamvuyonse akudalitse iwe, akubalitse iwe, akuchulukitse iwe, kuti ukhale khamu la anthu: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Mulungu Wamphamvuyonse akudalitse iwe, akubalitse iwe, akuchulukitse iwe, kuti ukhale khamu la anthu: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mulungu Mphambe adalitse ukwati wako, ndipo akupatse ana ochuluka, kuti udzakhale gulu lalikulu la mitundu yambiri ya anthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Mulungu Wamphamvuzonse akudalitse iwe nakupatse ana ambiri mpaka udzasanduke gulu lalikulu la mitundu ya anthu. Onani mutuwo |