Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 27:9 - Buku Lopatulika

9 Pitatu kubusa, ukanditengere ine kumeneko tiana tiwiri tabwino tambuzi; ndikonzere nato chakudya chokolera cha atate wako chonga chomwe achikonda:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Pitatu kubusa, ukanditengere ine kumeneko tiana tiwiri tabwino tambuzi; ndikonzere nato chakudya chokolera cha atate wako chonga chomwe achikonda:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Pita ku khola, ukanditengere timbuzi tiŵiri tonenepa bwino, kuti ndiphike, ndi kukonza chakudya chimene bambo wako amachikonda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Pita ku khola, ukatenge ana ambuzi abwino awiri, kuti ndikonzere abambo ako chakudya chokoma monga amakondera.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 27:9
6 Mawu Ofanana  

ndipo udzapita nacho kwa atate wako, kuti adye, ndi kukudalitsa iwe asanafe.


Ndipo anamuka nakatenga nadza nato kwa amake; amake ndipo anakonza chakudya chokolera chonga chimene anachikonda atate wake.


nundikonzere ine chakudya chokolera chonga chomwe ndichikonda ine, nudze nacho kwa ine kuti ndidzadye; kuti moyo wanga ukadalitse iwe ndisanafe.


Tsopanotu mwana wanga, tamvera mau anga monga momwe nditi ndikuuze iwe.


Ndipo Manowa anati kwa mthenga wa Yehova, Tiloleni tikuchedwetseni kuti tikukonzereni mwanawambuzi.


Ndipo Yese anatenga bulu namsenza mkate, ndi thumba la vinyo, ndi mwanawambuzi, nazitumiza kwa Saulo ndi Davide mwana wake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa