Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 27:10 - Buku Lopatulika

10 ndipo udzapita nacho kwa atate wako, kuti adye, ndi kukudalitsa iwe asanafe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 ndipo udzapita nacho kwa atate wako, kuti adye, ndi kukudalitsa iwe asanafe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Ukapereke chakudyacho kwa bambo wako kuti akadye, ndipo akudalitse asanafe.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Kenaka upite nacho chakudyacho kwa abambo ako kuti adye ndi kukudalitsa asanafe.”

Onani mutuwo Koperani




Genesis 27:10
3 Mawu Ofanana  

Ndipo anati, Yehova, Mulungu wa mbuyanga Abrahamu mundiyendetse ine bwino lero lino, mumchitire ufulu mbuyanga Abrahamu.


Yakobo ndipo anati kwa Rebeka amake, Taonani, Esau mkulu wanga ndiye munthu waubweya, ine ndine munthu wosalala.


Pitatu kubusa, ukanditengere ine kumeneko tiana tiwiri tabwino tambuzi; ndikonzere nato chakudya chokolera cha atate wako chonga chomwe achikonda:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa