Genesis 27:11 - Buku Lopatulika11 Yakobo ndipo anati kwa Rebeka amake, Taonani, Esau mkulu wanga ndiye munthu waubweya, ine ndine munthu wosalala. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Yakobo ndipo anati kwa Rebeka amake, Taonani, Esau mkulu wanga ndiye munthu waubweya, ine ndine munthu wosalala. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Koma Yakobe adauza mai wake kuti, “Mukudziŵa kuti Esau ndi wacheya, koma ine khungu langa ndi losalala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Koma Yakobo anati kwa Rebeka amayi ake, “Komatu mʼbale wanga Esau ndi munthu wa khungu la ubweya zedi, ndipo ine ndine munthu wa khungu losalala. Onani mutuwo |