Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 27:44 - Buku Lopatulika

44 ukhale naye masiku akuwerengeka, mpaka utamchokera ukali mkulu wako;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

44 ukhale naye masiku akuwerengeka, mpaka wamchokera ukali wa mkulu wako;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

44 Bakakhala kwa iyeyo kanthaŵi ndithu,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

44 Ukakhale naye kwa kanthawi mpaka mkwiyo wa mʼbale wako utatsika.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 27:44
3 Mawu Ofanana  

Zaka makumi awiriwo ndakhala nawe, nkhosa ndi mbuzi zako zazikazi sizinapoloze, ndi abira a zoweta zako sindinadye.


Ndinakhala chotere zaka makumi awiri m'nyumba mwako; zaka khumi ndi zinai ndinakutumikira iwe chifukwa cha ana ako aakazi awiri, ndi zaka zisanu ndi chimodzi chifukwa cha zoweta zako; wasintha malipiro anga kakhumi.


Pakuti Ambuye Yehova wa makamu ndiye amene akhudza dziko, nilisungunuka; ndi onse okhalamo adzachita maliro; ndipo lidzakwera lonseli ngati madzi a m'mtsinje; nilidzatsikanso ngati mtsinje wa mu Ejipito;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa