Genesis 27:42 - Buku Lopatulika42 Ndipo anauza Rebeka mau a Esau mwana wake wamkulu: ndipo iye anatumiza naitana Yakobo mwana wake wamng'ono, nati kwa iye, Taona, mkulu wako Esau, kunena za iwe, adzitonthoza yekha mtima wake kuti adzakupha iwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201442 Ndipo anauza Rebeka mau a Esau mwana wake wamkulu: ndipo iye anatumiza naitana Yakobo mwana wake wamng'ono, nati kwa iye, Taona, mkulu wako Esau, kunena za iwe, adzitonthoza yekha mtima wake kuti adzakupha iwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa42 Koma Rebeka atamva za maganizo onse a Esau, adaitana Yakobe namuuza kuti, “Taona, mbale wako Esau akuganiza zoti akuphe kuti akulipsire. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero42 Pamene Rebeka anamva zimene mwana wake wamkulu Esau ankaganiza, anayitanitsa Yakobo nati kwa iye, “Mʼbale wako Esau akulingalira zakuti akuphe kuti akulipsire. Onani mutuwo |