Genesis 27:32 - Buku Lopatulika32 Ndipo Isaki atate wake anati kwa iye, Ndiwe yani? Ndipo iye anati, Ndine mwana wanu woyamba Esau. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Ndipo Isaki atate wake anati kwa iye, Ndiwe yani? Ndipo iye anati, Ndine mwana wanu woyamba Esau. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Isaki adamufunsa kuti, “Kodi iwenso ndiwe yani?” Iye adayankha kuti, “Ndine mwana wanu wamkulu Esau.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Abambo ake, Isake, anamufunsa kuti, “Ndiwe yani?” Iye anayankha, “Ndine mwana wanu woyamba Esau.” Onani mutuwo |