Genesis 27:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo iyenso anakonza chakudya chokolera, nadza nacho kwa atate wake, nati kwa atate wake, Auke atate wanga, adye nyama ya mwana wake, kuti moyo wanu undidalitse ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo iyenso anakonza chakudya chokolera, nadza nacho kwa atate wake, nati kwa atate wake, Auke atate wanga, adye nyama ya mwana wake, kuti moyo wanu undidalitse ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Iyenso adaphika chakudya chabwino kwambiri, nakapereka kwa bambo wake. Esauyo adati, “Chonde bambo dzukani, khalani tsonga, mudye nyama imene ine mwana wanu ndakutengerani, ndipo mundidalitse.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Nayenso anakonza chakudya chokoma nabwera nacho kwa abambo ake. Ndipo anati kwa iye, “Chonde abambo, dzukani mukhale tsonga kuti mudye nyamayi ndi kuti mundidalitse.” Onani mutuwo |