Genesis 27:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo panali atatha Isaki kumdalitsa Yakobo, atatuluka Yakobo pamaso pa Isaki atate wake, Esau mkulu wake analowa kuchokera kuthengo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo panali atatha Isaki kumdalitsa Yakobo, atatuluka Yakobo pamaso pa Isaki atate wake, Esau mkulu wake analowa kuchokera kuthengo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Isaki atamaliza kudalitsako, Yakobe adachokapo. Nthaŵi yomweyo wafika Esau kuchokera kuuzimba kuja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Isake atatsiriza kudalitsa Yakobo, atangochoka pamaso pa abambo akewo, Esau anabwera kuchokera kosaka kuja. Onani mutuwo |