Genesis 27:17 - Buku Lopatulika17 ndipo anapereka m'dzanja la mwana wake Yakobo chakudya chokoleracho, ndi mikate imene anaipanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 ndipo anapereka m'dzanja la mwana wake Yakobo chakudya chokoleracho, ndi mikate imene anaipanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Ndipo adatenga buledi ndi chakudya chokonza bwino chija, napatsira Yakobe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Kenaka, anamupatsa Yakobo chakudya chokoma chija chimene anaphika pamodzi ndi buledi. Onani mutuwo |