Genesis 27:16 - Buku Lopatulika16 ndipo anaveka zikopa za tiana tambuzi pamanja ake ndi pakhosi pake posalala; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 ndipo anaveka zikopa za tiana tambuzi pamanja ake ndi pakhosi pake posalala; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Adamuvekanso zikopa za tianatambuzi pamikono pake ndiponso pakhosi pake posalala popanda cheya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Anamuvekanso manja ake ndi khosi lake ndi zikopa za mwana wambuzi. Onani mutuwo |