Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 27:15 - Buku Lopatulika

15 Ndipo Rebeka anatenga zovala zokoma za Esau mwana wake wamkulu zinali m'nyumba, naveka nazo Yakobo mwana wake wamng'ono;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Ndipo Rebeka anatenga zovala zokoma za Esau mwana wake wamkulu zinali m'nyumba, naveka nazo Yakobo mwana wake wamng'ono;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Pambuyo pake Rebeka adatenga zovala zabwino za Esau zimene ankazisunga m'nyumba, naveka mng'ono wake Yakobe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Tsono Rebeka anatenga zovala zabwino kwambiri za Esau mwana wake wamkulu zimene zinali mʼnyumba namuveka Yakobo.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 27:15
5 Mawu Ofanana  

Ndipo anamuka nakatenga nadza nato kwa amake; amake ndipo anakonza chakudya chokolera chonga chimene anachikonda atate wake.


ndipo anaveka zikopa za tiana tambuzi pamanja ake ndi pakhosi pake posalala;


Ndipo anasendera nampsompsona; ndipo anamva kununkhira kwa zovala zake, namdalitsa, nati, Taona, kununkhira kwa mwana wanga, kufanana ndi kununkhira kwa munda anaudalitsa Yehova;


Koma atateyo ananena kwa akapolo ake, Tulutsani msanga mwinjiro wokometsetsa, nimumveke; ndipo mpatseni mphete kudzanja lake ndi nsapato kumapazi ake;


Chenjerani nao alembi, amene afuna kuyendayenda ovala miinjiro, nakonda kupatsidwa moni m'misika, ndi mipando yaulemu m'sunagoge, ndi malo aulemu pamaphwando;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa