Genesis 27:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo anamuka nakatenga nadza nato kwa amake; amake ndipo anakonza chakudya chokolera chonga chimene anachikonda atate wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo anamuka nakatenga nadza nato kwa amake; amake ndipo anakonza chakudya chokolera chonga chimene anachikonda atate wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Choncho Yakobe adapita kukatenga timbuzito nakapatsa mai wake, ndipo Rebeka adaphika chakudya chimene bamboyo ankachikonda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Choncho anapita nakatenga timbuzito ndi kubwera nato kwa amayi ake. Choncho Rebeka anaphika chakudya chokoma monga momwe Isake amakondera. Onani mutuwo |