Genesis 27:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo amake anati kwa iye, Pa ine likhale temberero lako mwana wanga; koma tamvera mau anga, kazimuka kunditengera timeneto. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo amake anati kwa iye, Pa ine likhale temberero lako mwana wanga; koma tamvera mau anga, kazimuka kunditengera timeneto. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Mai wake adayankha kuti, “Mwana wanga, temberero lakelo lidzagwere ine, osati iwe. Iweyo ungochita zimene ndakuuza, kanditengere timbuzito.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Amayi ake anati kwa iye, “Mwana wanga, temberero limenelo ligwere ine. Iwe ungochita zimene ine ndikukuwuza; pita kanditengere timbuzito.” Onani mutuwo |