Genesis 27:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo iye analowa kwa atate wake, nati, Atate wanga; iye anati, Ndine pano; ndani iwe mwana wanga? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo iye analowa kwa atate wake, nati, Atate wanga; iye anati, Ndine pano; ndani iwe mwana wanga? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Yakobe adapita kwa bambo wake, namuitana kuti, “Bambo!” Isaki adafunsa kuti, “Kodi ndiwe mwana wanga uti?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Yakobo anapita kwa abambo ake ndipo anati, “Abambo anga.” Ndipo anayankha, “Eya, kodi ndiwe mwana wanga uti?” Onani mutuwo |