Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 26:35 - Buku Lopatulika

35 Ndipo iwo anapweteka mtima wa Isaki ndi wa Rebeka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

35 ndipo iwo anapweteka mtima wa Isaki ndi wa Rebeka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

35 Onseŵa adapezetsa Isaki ndi Rebeka mavuto aakulu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

35 Akazi awiriwa anasandutsa Isake ndi Rebeka kukhala ndi moyo wa madandawulo nthawi zonse.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 26:35
5 Mawu Ofanana  

ndipo ndidzakulumbiritsa iwe pa Yehova, Mulungu wa Kumwamba, ndi Mulungu wa dziko lapansi, kuti usadzamtengere mwana wanga mkazi wa kwa ana aakazi a Akananiwo, amene ndikhala pakati pao.


Ndipo anati Rebeka kwa Isaki, Ndalema moyo wanga chifukwa cha ana aakazi a Ahiti, akatenga Yakobo mkazi wa ana aakazi a Ahiti, onga ana aakazi a m'dziko lino, moyo wanga udzandikhalira ine bwanji?


ndipo Esau anaona kuti ana aakazi a Kanani sanakondweretse Isaki atate wake:


kuti ana aamuna a Mulungu anayang'ana ana aakazi a anthu, kuti iwo anali okongola; ndipo anadzitengera okha akazi onse amene anawasankha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa