Genesis 26:34 - Buku Lopatulika34 Pamene Esau anali wa zaka makumi anai, anakwatira Yuditi mwana wamkazi wa Beeri Muhiti, ndi Basemati mwana wamkazi wa Eloni Muhiti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Pamene Esau anali wa zaka makumi anai, anakwatira Yuditi mwana wamkazi wa Beeri Muhiti, ndi Basemati mwana wamkazi wa Eloni Muhiti: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Pamene Esau anali wa zaka makumi anai, adakwatira Yuditi mwana wa Beeri Muhiti. Adakwatiranso Basemati, mwana wa Eloni Muhiti. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Pamene Esau anali ndi zaka 40, anakwatira Yuditi mwana wamkazi wa Beeri Mhiti. Anakwatiranso Basemati mwana wa mkazi wa Eloni Mhiti. Onani mutuwo |