Genesis 26:32 - Buku Lopatulika32 Ndipo panali tsiku lomwelo anyamata ake a Isaki anadza namuuza iye za chitsime chimene anakumba, nati kwa iye, Tapeza madzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Ndipo panali tsiku lomwelo anyamata ake a Isaki anadza namuuza iye za chitsime chimene anakumba, nati kwa iye, Tapeza madzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Tsiku limenelo antchito ake a Isaki adabwera kudzamuuza za chitsime chimene iwowo adaakumba. Adati, “Tapeza madzi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Tsiku limenelo, antchito a Isake anabwera namuwuza za chitsime chimene anakumba. Iwo anati, “Tawapeza madzi!” Onani mutuwo |