Genesis 26:28 - Buku Lopatulika28 Ndipo iwo anati, Kuona tinaona kuti Yehova ali ndi iwe; ndipo tinati, Tilumbiriranetu tonse awiri, ife ndi iwe, tichite pangano ndi iwe; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndipo iwo anati, Kuona tinaona kuti Yehova ali ndi iwe; ndipo tinati, Tilumbiriranetu tonse awiri, ife ndi iwe, tichite pangano ndi iwe; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Iwowo adayankha kuti, “Tsopano tikudziŵa kuti Chauta ali nanu, ndipo taganiza zoti inu ndi ife tichite chipangano. Tikufuna kuti inu mulonjeze Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Iwo anayankha, “Tsopano tadziwa kuti Yehova anali ndi iwe; ndiye taganiza kuti inu ndi ife tichite lumbiro. Ife tichite pangano ndi inu Onani mutuwo |