Genesis 26:27 - Buku Lopatulika27 Ndipo Isaki anati kwa iwo, Mwandidzera chifukwa chiyani, inu akundida ine, ndi kundichotsa kwanu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndipo Isaki anati kwa iwo, Mwandidzera chifukwa chiyani, inu akundida ine, ndi kundichotsa kwanu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Tsono Isaki adaŵafunsa kuti, “Kodi chifukwa chiyani mwabwera kuno kudzandiwona, pamene kale mudaandiwonetsa mtima woipa mpaka kundichotsa m'dziko mwanu?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Tsopano Isake anawafunsa kuti, “Bwanji mwabwera kwa ine, popeza munandichitira nkhanza ndi kundithamangitsa?” Onani mutuwo |