Genesis 26:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo ananka kwa iye Abimeleki kuchokera ku Gerari, ndi Ahuzati bwenzi lake, ndi Fikolo, kazembe wa nkhondo yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo ananka kwa iye Abimeleki kuchokera ku Gerari, ndi Ahuzati bwenzi lake, ndi Fikolo, kazembe wa nkhondo yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Abimeleki adachoka ku Gerari nabwera kudzacheza ndi Isaki pamodzi ndi Ahuzati, nduna yake, ndi Fikolo mtsogoleri wa ankhondo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Abimeleki pamodzi ndi Ahuzati mlangizi wake ndi Fikolo mkulu wa ankhondo ake anabwera kwa Isake kuchokera ku Gerari. Onani mutuwo |