Genesis 26:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo panali njala padzikopo, yoyenjezeka ndi njala yoyamba ija imene inali masiku a Abrahamu, ndipo Isaki ananka kwa Abimeleki mfumu ya Afilisti ku Gerari. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo panali njala padzikopo, yoyenjezeka ndi njala yoyamba ija imene inali masiku a Abrahamu, ndipo Isaki ananka kwa Abimeleki mfumu ya Afilisti ku Gerari. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 M'dzikomo mudaloŵanso njala kuwonjezera pa imene idaaloŵa pa nthaŵi ya Abrahamu. Ndipo Isaki adapita kwa Abimeleki mfumu ya Afilisti ku Gerari. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Tsono kunagwa njala ina mʼdzikomo kuwonjezera pa ija ya poyamba ya nthawi ya Abrahamu ndipo Isake anapita kwa Abimeleki mfumu ya Afilisti ku Gerari. Onani mutuwo |