Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 25:12 - Buku Lopatulika

12 Mibadwo ya Ismaele mwana wamwamuna wa Abrahamu, amene Hagara Mwejipito mdzakazi wa Sara anambalira Abrahamu ndi iyi:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Mibadwo ya Ismaele mwana wamwamuna wake wa Abrahamu, amene Hagara Mwejipito mdzakazi wa Sara anambalira Abrahamu ndi iyi:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Nazi zidzukulu za Ismaele, mwana wa Abrahamu amene adamubalira Hagara, mdzakazi wa ku Ejipito uja.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Nazi zidzukulu za Ismaeli, mwana wa Abrahamu amene wantchito wa Sara, Hagara Mwigupto uja, anaberekera Abrahamu.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 25:12
8 Mawu Ofanana  

Koma za Ismaele, ndamvera iwe: taona, ndamdalitsa iye, ndipo ndidzamchulukitsa iye ndithu; adzabala akalonga khumi ndi awiri, ndipo ndidzamuyesa iye mtundu waukulu.


Ndipo mwana wamwamuna wa mdzakazi uyo ndidzayesa mtundu, chifukwa iye ndiye mbeu yako.


Tauka, nuukitse mnyamatayo, ndi kumgwira m'dzanja lako; chifukwa ndidzamuyesa iye mtundu waukulu.


Ana a Abrahamu: Isaki, ndi Ismaele.


Mibadwo yao ndi awa; woyamba wa Ismaele Nebayoti; ndi Kedara ndi Adibeele, ndi Mibisamu,


Mahema a Edomu ndi a Aismaele; Mowabu ndi Ahagiri;


Gideoni anatinso kwa iwo, Mundilole ndipemphe kanthu kamodzi kwa inu, mundipatse aliyense maperere mwa zofunkha zanu; pakuti anali nao maperere agolide, pokhala anali Aismaele.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa