Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 25:13 - Buku Lopatulika

13 ndipo maina a ana a Ismaele, maina ao m'mibadwo yao ndi awa: woyamba wa Ismaele ndi Nebayoti; ndi Kedara, ndi Adibeele, ndi Mibisamu,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 ndipo maina a ana a Ismaele, maina ao m'mibadwo yao ndi awa: woyamba wa Ismaele ndi Nebayoti; ndi Kedara, ndi Adibeele, ndi Mibisamu,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Maina a ana a Ismaele ndi aŵa: woyamba anali Nebayoti, pambuyo pake adabereka Kedara, Adibeele, Mibisamu,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Awa ndi mayina a ana a Ismaeli monga mwa mndandanda wa mabadwidwe awo: Nebayoti ndiye anali mwana woyamba wa Ismaeli; kenaka Kedara, Adibeeli, Mibisamu,

Onani mutuwo Koperani




Genesis 25:13
14 Mawu Ofanana  

Koma za Ismaele, ndamvera iwe: taona, ndamdalitsa iye, ndipo ndidzamchulukitsa iye ndithu; adzabala akalonga khumi ndi awiri, ndipo ndidzamuyesa iye mtundu waukulu.


ndi Misima, ndi Duma, ndi Masa;


ndipo Esau ananka kwa Ismaele, naonjezera kwa akazi amene anali nao, natenga Mahalati mwana wamkazi wa Ismaele mwana wa Abrahamu, mlongo wake wa Nebayoti akhale mkazi wake.


ndi Basemati mwana wamkazi wa Ismaele, mlongo wake wa Nebayoti.


Tsoka ine, kuti ndili mlendo mu Meseki, kuti ndigonera m'mahema a Kedara!


Wakuda ine, koma wokongola, ana aakazinu a ku Yerusalemu, ngati mahema a Kedara, ngati nsalu zotchinga za Solomoni.


Chipululu ndi mizinda yake ikweze mau ao, midzi imene Kedara akhalamo; okhala mu Sela aimbe, akuwe kuchokera pamwamba pa mapiri.


Zoweta za Kedara zidzasonkhana kwa iwe, nkhosa zamphongo za Nebayoti zidzakutumikira; izo zidzafika ndi kulandiridwa paguwa langa la nsembe; ndipo ndidzakometsa nyumba ya ulemerero wanga.


Pakuti pitani ku zisumbu za Kitimu nimuone; tumizani ku Kedara nimulingalire bwino; nimuone ngati chinalipo chotere.


Za Kedara, ndi za maufumu a Hazori, amene anawakantha Nebukadinezara mfumu ya ku Babiloni. Yehova atero: Ukani, kwerani ku Kedara, funkhani ana a ku m'mawa.


Arabiya ndi akalonga onse a ku Kedara anazolowerana nao malonda ako; anaankhosa, nkhosa zamphongo, ndi mbuzi, izi anagulana nawe.


Gideoni anatinso kwa iwo, Mundilole ndipemphe kanthu kamodzi kwa inu, mundipatse aliyense maperere mwa zofunkha zanu; pakuti anali nao maperere agolide, pokhala anali Aismaele.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa