Genesis 24:39 - Buku Lopatulika39 Ndipo ndinati kwa mbuyanga, Kapena mkazi sadzanditsata ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Ndipo ndinati kwa mbuyanga, Kapena mkazi sadzanditsata ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Ndipo ine ndidamuyankha mbuyanga kuti, ‘Nanga zidzatani ngati mkaziyo adzakana kubwera nane kuno?’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 “Ndipo ine ndinati kwa mbuye wanga, ‘Nanga mkaziyo akakapanda kubwera nane pamodzi?’ Onani mutuwo |