Genesis 24:38 - Buku Lopatulika38 koma udzanke kunyumba ya atate wanga, kwa abale anga, ndi kumtengera mwana wanga mkazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 koma udzanke kunyumba ya atate wanga, kwa abale anga, ndi kumtengera mwana wanga mkazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Koma upite kwathu kwa atate anga ndi achibale anga, kukamutengera mkazi mwana wanga kumeneko.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 koma upite ku banja la abambo anga ndi kwa abale anga kuti ukamupezere mkazi mwana wanga.’ ” Onani mutuwo |