Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 24:37 - Buku Lopatulika

37 Ndipo mbuyanga anandilumbiritsa ine kuti, Usamtengere mwana wanga mkazi wa ana aakazi a Kanani, m'dziko mwao m'mene ndikhala ine;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

37 Ndipo mbuyanga anandilumbiritsa ine kuti, Usamtengere mwana wanga mkazi wa ana akazi a Kanani, m'dziko mwao m'mene ndikhala ine;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

37 Tsono mbuyanga adandilumbiritsa kuti ndisunge mau ake akuti, ‘Mwana wangayu usadzamfunire mbeta pakati pa anamwali a dziko lino la Kanani, kumene ndili ine kuno.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

37 Tsono mbuye wanga anandilumbiritsa kuti ndisunge mawu ake akuti, ‘Usadzamupezere mwana wanga mkazi kuchokera mwa atsikana a dziko lino la Kanaani,

Onani mutuwo Koperani




Genesis 24:37
5 Mawu Ofanana  

koma udzanke kunyumba ya atate wanga, kwa abale anga, ndi kumtengera mwana wanga mkazi.


Ndipo anati Rebeka kwa Isaki, Ndalema moyo wanga chifukwa cha ana aakazi a Ahiti, akatenga Yakobo mkazi wa ana aakazi a Ahiti, onga ana aakazi a m'dziko lino, moyo wanga udzandikhalira ine bwanji?


kuti ana aamuna a Mulungu anayang'ana ana aakazi a anthu, kuti iwo anali okongola; ndipo anadzitengera okha akazi onse amene anawasankha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa