Genesis 24:36 - Buku Lopatulika36 Ndipo Sara mkazi wake wa mbuyanga anambalira mbuyanga mwana wamwamuna, mkaziyo anali wokalamba; ndipo anampatsa mwanayo zonse ali nazo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Ndipo Sara mkazi wake wa mbuyanga anambalira mbuyanga mwana wamwamuna, mkaziyo anali wokalamba; ndipo anampatsa mwanayo zonse ali nazo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Sara, mkazi wake wa mbuyanga, adamubalira mwana wamwamuna, Sarayo atakalamba kale. Ndipo mbuyangayo wamupatsa chuma chake chonse mwana ameneyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Sara, mkazi wa mbuye wanga anamubalira iye mwana wamwamuna ngakhale kuti Sarayo anali wokalamba. Tsono mbuye wanga wamupatsa mwanayo chuma chonse. Onani mutuwo |