Genesis 24:25 - Buku Lopatulika25 Natinso kwa iye, Tili nao udzu ndi zakudya zambiri ndi malo ogona. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Natinso kwa iye, Tili nao udzu ndi zakudya zambiri ndi malo ogona. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 “Chakudya chodyetsa nyamazi chiliko kwathu, ndipo malo oti inu mugoneko aliponso.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Ndipo anapitiriza kunena kuti, “Chakudya chodyetsa nyamazi chilipo kwathu ndipo malo woti mugone aliponso.” Onani mutuwo |