Genesis 24:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo anafulumira nathira madzi a m'mtsuko wake m'chomwera, nathamangiranso kuchitsime kukatunga, nazitungira ngamira zake zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo anafulumira nathira madzi a m'mtsuko wake m'chomwera, nathamangiranso kuchitsime kukatunga, nazitungira ngamira zake zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Pompo madzi amumtsukowo adaŵatsanyulira m'chomwera nyama, nabwerera ku chitsime kukatenga madzi ena oti amwetse ngamirazo mpaka zitakwana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Choncho anafulumira kukhuthula madzi a mu mtsuko aja momwera ziweto, nathamanga kubwerera ku chitsime kukatunga madzi ena, ndipo anatunga okwanira ngamira zake zonse. Onani mutuwo |