Genesis 24:19 - Buku Lopatulika19 Atatha kumwetsa iye, anati, Ndidzatungiranso ngamira zako, mpaka zitamwa zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Atatha kumwetsa iye, anati, Ndidzatungiranso ngamira zako, mpaka zitamwa zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Mlendo uja atamwa madziwo, namwaliyo adati, “Ndibwera nawonso madzi, kuti zimwe ngamira zanu mpaka zikwane.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Atatha kupereka madzi akumwa kwa mlendo uja, mtsikanayo anati, “Ndikatungiranso ngamira madzi kuti zimwe mpaka zitakwana.” Onani mutuwo |