Genesis 24:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo anati, Imwa mbuyanga; nafulumira nayangata mtsuko m'manja mwake namwetsa iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo anati, Imwa mbuyanga; nafulumira nayangata mtsuko m'manja mwake namwetsa iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Namwaliyo adati, “Imwani mbuyanga,” ndipo mosachedwa adatsitsa mtsuko wake uja pa phewa, naugwirira kuti mlendoyo amwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Mtsikanayo anati, “Imwani mbuye wanga.” Ndipo mofulumira anatsitsa mtsuko uja nawuyika mʼmanja ndi kumupatsa kuti amwe. Onani mutuwo |