Genesis 24:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo mnyamatayo anamthamangira kukomana naye, nati, Ndimwetu madzi pang'ono a m'mtsuko mwako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo mnyamatayo anamthamangira kukomana naye, nati, Ndimwetu madzi pang'ono a m'mtsuko mwako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Tsono wantchito uja adamthamangira kuti akakumane naye, nampempha kuti, “Chonde mundipatseko madzi a mumtsuko mwanu kuti ndimwe.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Wantchito uja anathamanga kukakumana naye nati, “Chonde patseko madzi pangʼono a mu mtsuko wakowo kuti ndimwe.” Onani mutuwo |