Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 24:21 - Buku Lopatulika

21 Munthuyo ndipo anamyang'anira iye, nakhala chete, kuti adziwe ngati Yehova anamuyendetsa bwino kapena iai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Munthuyo ndipo anamyang'anira iye, nakhala chete, kuti adziwe ngati Yehova anamuyendetsa bwino kapena iai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Munthu uja anali phee, kuyang'ana zimene ankachita namwaliyo, kuti aone ngati Chauta wadalitsa ulendo wake kapena ai.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Modekha, munthu uja anayangʼanitsitsa kwambiri mtsikana uja kuti adziwedi ngati Yehova anamutsogolera pa ulendo wake uja kapena ayi.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 24:21
13 Mawu Ofanana  

Ndipo anati, Yehova, Mulungu wa mbuyanga Abrahamu mundiyendetse ine bwino lero lino, mumchitire ufulu mbuyanga Abrahamu.


Ndipo anafulumira nathira madzi a m'mtsuko wake m'chomwera, nathamangiranso kuchitsime kukatunga, nazitungira ngamira zake zonse.


Ndipo anati, Ayamikike Yehova Mulungu wa Ambuyanga Abrahamu amene sanasiye mbuyanga wopanda chifundo chake ndi zoona zake: koma ine Yehova wanditsogolera m'njira ya kunyumba ya abale ake a mbuyanga.


Ndipo iye anati kwa iwo, Musandichedwetse ine, pakuti Yehova wandiyendetsa bwino m'njira yanga: mundilole ine ndinke kwa mbuyanga.


Yamikani Yehova pakuti Iye ndiye wabwino; pakuti chifundo chake nchosatha.


Ayamike Yehova chifukwa cha chifundo chake, ndi zodabwitsa zake za kwa ana a anthu!


Wokhala nazo nzeru asamalire izi, ndipo azindikire zachifundo za Yehova.


Ayamike Yehova chifukwa cha chifundo chake, ndi zodabwitsa zake za kwa ana a anthu!


Koma Maria anasunga mau awa onse, nawalingalira mumtima mwake.


Ndipo anatsika nao pamodzi nadza ku Nazarete; nawamvera iwo: ndipo amake anasunga zinthu izi zonse mumtima mwake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa