Genesis 22:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo mkazi wake wamng'ono, dzina lake Reuma, iyenso anabala Teba, ndi Gahamu, ndi Tahasi, ndi Maaka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo mkazi wake wamng'ono, dzina lake Reuma, iyenso anabala Teba, ndi Gahamu, ndi Tahasi, ndi Maaka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Ndipo Reuma, mzikazi wa Nahori, adabala Teba, Gahamu, Tahasi ndi Maaka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Mkazi wake wachiwiri, dzina lake Reuma, anamubaliranso Nahori ana awa: Teba, Gahamu, Tahasi ndi Maaka. Onani mutuwo |