Genesis 23:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Sara anali wa zaka zana limodzi kudza makumi awiri ndi zisanu ndi ziwiri: ndizo zaka za moyo wa Sara. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Sara anali wa zaka zana limodzi kudza makumi awiri ndi zisanu ndi ziwiri: ndizo zaka za moyo wa Sara. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Sara adakhala ndi moyo zaka 127, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Sara anakhala ndi moyo zaka 127. Onani mutuwo |