Genesis 22:23 - Buku Lopatulika23 Ndimo Betuele anabala Rebeka: amenewa asanu ndi atatu Milika anambalira Nahori mphwake wa Abrahamu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndimo Betuele anabala Rebeka: amenewa asanu ndi atatu Milika anambalira Nahori mphwake wa Abrahamu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Betuele adabereka Rebeka. Milika adabalira Nahori mbale wa Abrahamu ana asanu ndi atatu ameneŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Betueli anabereka Rebeka. Milika anaberekera Nahori, mʼbale wake wa Abrahamu, ana aamuna asanu ndi atatu amenewa. Onani mutuwo |