Genesis 22:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo Abrahamu anabwera kwa anyamata ake, ndipo anauka nayenda pamodzi kumuka ku Beereseba; ndipo anakhala Abrahamu pa Beereseba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo Abrahamu anabwera kwa anyamata ake, ndipo anauka nayenda pamodzi kumuka ku Beereseba; ndipo anakhala Abrahamu pa Beereseba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Abrahamu adabwerera kumene adaasiya antchito ake kuja, ndipo onsewo adapita ku Beereseba. Tsono Abrahamu adakhazikika komweko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Kenaka Abrahamu anabwerera kumene anasiya antchito ake kuja nanyamukira nawo pamodzi kupita ku Beeriseba. Ndipo Abrahamu anakhala ku Beeriseba. Onani mutuwo |