Genesis 21:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo Abrahamu anali wa zaka zana limodzi pamene anambadwira iye Isaki mwana wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo Abrahamu anali wa zaka zana limodzi pamene anambadwira iye Isaki mwana wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Abrahamu nkuti ali wa zaka 100 pamene Isakiyo adabadwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Abrahamu anali ndi 100 pamene mwana wake Isake anabadwa. Onani mutuwo |