Genesis 21:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Sara anati, Mulungu anandisekeretsa ine; onse akumva adzasekera pamodzi ndi ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Sara anati, Mulungu anandisekeretsa ine; onse akumva adzasekera pamodzi ndi ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Tsono Sara adati, “Mulungu wandikondweretsa ndi kundiseketsa. Aliyense amene adzamve zimenezi, adzakondwera nane.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Sara anati, “Mulungu wandibweretsera mseko, ndipo aliyense amene adzamva zimenezi adzaseka nane pamodzi.” Onani mutuwo |