Genesis 21:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo Abrahamu anamdula mwana wake wamwamuna Isaki pamene anali wa masiku ake asanu ndi atatu, monga Mulungu anamlamulira iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo Abrahamu anamdula mwana wake wamwamuna Isaki pamene anali wa masiku ake asanu ndi atatu, monga Mulungu anamlamulira iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Abrahamu adamuumbala mwanayo ali wa masiku asanu ndi atatu, monga momwe Mulungu adaalamulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Isake atakwanitsa masiku asanu ndi atatu, Abrahamu anamuchita mdulidwe monga Mulungu anamulamulira. Onani mutuwo |