Genesis 21:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo Abrahamu anamutcha dzina lake la mwana wake wamwamuna amene anabala iye, amene anambalira iye Sara, Isaki. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo Abrahamu anamutcha dzina lake la mwana wake wamwamuna amene anabala iye, amene anambalira iye Sara, Isaki. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ndipo mwana wa Abrahamuyo, mwana amene Sara adamubalirayo, Abrahamu adamutcha Isaki. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Abrahamu anapereka dzina loti Isake kwa mwana wamwamuna amene Sara anamuberekera. Onani mutuwo |