Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 21:29 - Buku Lopatulika

29 Ndipo Abimeleki anati kwa Abrahamu, Nanga anaankhosa aakazi asanu ndi awiri amene wapatula pa okha?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

29 Ndipo Abimeleki anati kwa Abrahamu, Nanga anaankhosa akazi asanu ndi awiri amene wapatula pa okha?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

29 Abimeleki adamufunsa kuti “Chifukwa chiyani mukuchita zimenezi?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

29 ndipo Abimeleki anafunsa Abrahamu, “Kodi tanthauzo lake la ana ankhosa aakazi asanu ndi awiri amene wawapatula pawokhawa nʼchiyani?”

Onani mutuwo Koperani




Genesis 21:29
5 Mawu Ofanana  

Ndipo Abrahamu anapatula anaankhosa aakazi asanu ndi awiri pa okha.


Ndipo anati, Anaankhosa aakazi asanu ndi awiriwa uwalandire padzanja langa, kuti akhale mboni zanga, kuti ndakumba ine chitsime chimenechi.


Ndipo anati, Nanga khamu lonse limene ndinakomana nalo nlotani? Ndipo anati, Kuti ndipeze ufulu pamaso pa mbuyanga.


Ndipo kudzakhala, pamene ana anu adzanena ndi inu, Kutumikiraku muli nako nkutani?


Ndipo Samuele anati, Koma tsono kulirako kwa nkhosa ndilikumva m'makutu anga, ndi kulirako kwa ng'ombe ndilikumva, nchiyani?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa