Genesis 21:28 - Buku Lopatulika28 Ndipo Abrahamu anapatula anaankhosa aakazi asanu ndi awiri pa okha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndipo Abrahamu anapatula anaankhosa akazi asanu ndi awiri pa okha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Abrahamu adapatulako anaankhosa asanu ndi aŵiri kuchotsa pa zoŵeta zake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Abrahamu anapatulako ana ankhosa aakazi asanu ndi awiri kuchoka pagulu la nkhosa zina, Onani mutuwo |