Genesis 21:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Yehova anayang'anira Sara monga momwe anati, ndipo Yehova anamchitira iye monga ananena. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Yehova anayang'anira Sara monga momwe anati, ndipo Yehova anamchitira iye monga ananena. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Chauta adakumbukira Sara namchitira zimene adaamulonjeza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yehova anakomera mtima Sara monga ananenera, ndipo Yehovayo anachita monga momwe analonjezera. Onani mutuwo |