Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 2:6 - Buku Lopatulika

6 koma inakwera nkhungu yotuluka padziko lapansi, nkuthirira ponse pamwamba panthaka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 koma inakwera nkhungu yotuluka pa dziko lapansi, niithirira ponse pamwamba pa nthaka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Koma madzi ankatuluka m'dziko lonse lapansi ndi kumathirira nthaka.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 koma kasupe ankatuluka mʼnthaka ndi kuthirira pa dziko lonse.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 2:6
3 Mawu Ofanana  

Ndi zomera zonse za m'munda zisanakhale m'dziko lapansi, ndiponso matherere onse a m'munda asanamere; chifukwa Yehova Mulungu sanavumbitsire mvula padziko lapansi, ndipo panalibe munthu wakulima nthaka;


Ndipo Yehova Mulungu anaumba munthu ndi dothi lapansi, nauzira mpweya wa moyo m'mphuno mwake; munthuyo nakhala wamoyo.


Akweza mitambo ichokere ku malekezero a dziko lapansi; ang'animitsa mphezi zidzetse mvula; atulutsa mphepo mosungira mwake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa