Genesis 2:25 - Buku Lopatulika25 Onse awiri ndipo anali amaliseche, mwamuna ndi mkazi wake, ndipo analibe manyazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Onse awiri ndipo anali amaliseche, mwamuna ndi mkazi wake, ndipo analibe manyazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Mwamunayo ndi mkazi wake uja, onse anali maliseche, komabe sankachita manyazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Munthu uja ndi mkazi wakeyo, onse awiri anali maliseche ndipo analibe manyazi. Onani mutuwo |